1 Mafumu 6:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndipo mʼchaka cha 11, mwezi wa Buli,* (womwe ndi mwezi wa 8), anamaliza zinthu zonse panyumbayo mogwirizana ndi pulani yake.+ Choncho Solomo anamanga nyumbayo zaka 7. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:38 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), ptsa. 2138-2139, 2244
38 Ndipo mʼchaka cha 11, mwezi wa Buli,* (womwe ndi mwezi wa 8), anamaliza zinthu zonse panyumbayo mogwirizana ndi pulani yake.+ Choncho Solomo anamanga nyumbayo zaka 7.