-
1 Mafumu 7:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Nyumbayi inali yosanja kawiri. Nsanjika iliyonse inali ndi mzere wa mawindo. Choncho nyumba yonseyo inali ndi mizere itatu ya mawindo okhala ndi mafelemu. Mawindo a mbali ina anayangʼanizana ndi mawindo a mbali inanso ya nyumbayo.
-