-
1 Mafumu 7:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Kenako anamanga Khonde la Zipilala. Mulitali mwake linali mikono 50 ndipo mulifupi linali mikono 30. Kutsogolo kwa khondelo kunalinso kakhonde kena kokhala ndi zipilala ndi denga.
-