1 Mafumu 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anamanganso Bwalo la Mpando Wachifumu,+ kumene ankaweruzira milandu. Bwaloli linkatchedwa Bwalo Loweruzira Milandu.+ Makoma ake anawakuta ndi matabwa a mkungudza kuyambira pansi mpaka kudenga.
7 Anamanganso Bwalo la Mpando Wachifumu,+ kumene ankaweruzira milandu. Bwaloli linkatchedwa Bwalo Loweruzira Milandu.+ Makoma ake anawakuta ndi matabwa a mkungudza kuyambira pansi mpaka kudenga.