1 Mafumu 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nyumba zonsezi, kuyambira pamaziko ake mpaka pamwamba pa khoma, ndiponso kuchokera panja pa nyumbazo mpaka kubwalo lalikulu,+ zinamangidwa ndi miyala yokwera mtengo+ yochita kuyeza ndiponso yocheka ndi macheka a miyala, mkati ndi kunja komwe.
9 Nyumba zonsezi, kuyambira pamaziko ake mpaka pamwamba pa khoma, ndiponso kuchokera panja pa nyumbazo mpaka kubwalo lalikulu,+ zinamangidwa ndi miyala yokwera mtengo+ yochita kuyeza ndiponso yocheka ndi macheka a miyala, mkati ndi kunja komwe.