14 Mayi ake anali mkazi wamasiye wa fuko la Nafitali. Bambo ake anali a ku Turo odziwa kupanga zinthu zakopa.+ Hiramu anali waluso, womvetsa zinthu+ ndiponso wodziwa bwino ntchito yopanga zinthu zakopa. Iye anabwera kwa Mfumu Solomo ndipo anamugwirira ntchito yake yonse.