1 Mafumu 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamutu wa chipilala chilichonse anaikapo maukonde opangidwa ndi matcheni opotanapotana.+ Pamutu wina anaikapo ukonde wopangidwa ndi matcheni 7 ndipo pamutu winawo anaikaponso ukonde wopangidwa ndi matcheni 7.
17 Pamutu wa chipilala chilichonse anaikapo maukonde opangidwa ndi matcheni opotanapotana.+ Pamutu wina anaikapo ukonde wopangidwa ndi matcheni 7 ndipo pamutu winawo anaikaponso ukonde wopangidwa ndi matcheni 7.