1 Mafumu 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako anapanga mizere iwiri ya makangaza* kuzungulira maukonde awiri aja, nʼkuveka mitu imene inali pamwamba pa zipilalazo. Anachita zimenezi pamitu yonse iwiri.
18 Kenako anapanga mizere iwiri ya makangaza* kuzungulira maukonde awiri aja, nʼkuveka mitu imene inali pamwamba pa zipilalazo. Anachita zimenezi pamitu yonse iwiri.