1 Mafumu 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako iye anapanga thanki yosungira madzi.*+ Thankiyo inali yozungulira ndipo inali mikono 10 kuchokera mbali ina kufika ina, kuyeza modutsa pakati. Thankiyo inali yaitali mikono 5 ndipo kuzungulira thanki yonseyo inali mikono 30.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:23 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,
23 Kenako iye anapanga thanki yosungira madzi.*+ Thankiyo inali yozungulira ndipo inali mikono 10 kuchokera mbali ina kufika ina, kuyeza modutsa pakati. Thankiyo inali yaitali mikono 5 ndipo kuzungulira thanki yonseyo inali mikono 30.+