1 Mafumu 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kuchindikala kwa thankiyo kunali chikhatho* chimodzi. Milomo yake inali ngati kukamwa kwa mphika kapena ngati maluwa. Muthankiyo munkalowa madzi okwana mitsuko* 2,000. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:26 Nsanja ya Olonda,2/1/2008, tsa. 1512/1/2005, tsa. 19
26 Kuchindikala kwa thankiyo kunali chikhatho* chimodzi. Milomo yake inali ngati kukamwa kwa mphika kapena ngati maluwa. Muthankiyo munkalowa madzi okwana mitsuko* 2,000.