1 Mafumu 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anapanga zotengera 10+ zakopa zokhala ndi mawilo. Chotengera chilichonse chinali mikono 4 mulitali, mikono 4 mulifupi komanso mikono itatu kupita mʼmwamba.
27 Kenako anapanga zotengera 10+ zakopa zokhala ndi mawilo. Chotengera chilichonse chinali mikono 4 mulitali, mikono 4 mulifupi komanso mikono itatu kupita mʼmwamba.