29 Pamalata amene anali pakati pa zitsulo zopingasana anajambulapo mikango,+ ngʼombe zamphongo ndiponso akerubi.+ Pazitsulo zopingasana anajambulaponso zinthu zimenezi. Pamwamba ndi pansi pa mikango ndi ngʼombe zamphongozo, anajambulapo nkhata zamaluwa.