-
1 Mafumu 7:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Besenilo linali mkati mwa mbali yapamwamba ya chotengeracho ndipo kuchoka pansi kufika mumkombero linali mkono umodzi. Pakamwa pake panali pozungulira ndipo tikaphatikiza ndi mkomberowo, beseni lonse linali lalitali mkono umodzi ndi hafu. Mʼmbali mwa pakamwa pake anajambulamo zokongoletsera mochita kugoba. Malata amʼmbali mwake anali a mbali 4 zofanana, osati ozungulira.
-