-
1 Mafumu 7:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Pansi pa malata a mʼmbaliwo panali mawilo 4. Zogwiriziza za mawilowo anazilumikiza ku chotengeracho ndipo wilo lililonse linali lalitali mkono umodzi ndi hafu.
-