-
1 Mafumu 7:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Chotengera chilichonse chinali ndi makona 4, ndipo pakona iliyonse panali chogwiriziza. Zogwirizizazo anaziumbira kumodzi ndi chotengeracho.
-