1 Mafumu 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Patimafelemuto ndiponso pamalata amʼmbaliwo anajambulapo mochita kugoba akerubi, mikango komanso mitengo ya kanjedza mogwirizana ndi kukula kwa malo ake. Anajambulanso nkhata zamaluwa kuzungulira chokhazikapo besenicho.+
36 Patimafelemuto ndiponso pamalata amʼmbaliwo anajambulapo mochita kugoba akerubi, mikango komanso mitengo ya kanjedza mogwirizana ndi kukula kwa malo ake. Anajambulanso nkhata zamaluwa kuzungulira chokhazikapo besenicho.+