1 Mafumu 7:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Anaika zotengera 5 mbali yakumanja kwa nyumbayo komanso zotengera 5 mbali yakumanzere. Thanki ija anaiika kumanja kwa nyumbayo, kumʼmwera chakumʼmawa.+
39 Anaika zotengera 5 mbali yakumanja kwa nyumbayo komanso zotengera 5 mbali yakumanzere. Thanki ija anaiika kumanja kwa nyumbayo, kumʼmwera chakumʼmawa.+