1 Mafumu 7:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Hiramu+ anapanganso mabeseni, mafosholo+ ndi mbale zolowa.+ Choncho iye anamaliza ntchito yonse imene ankagwirira Mfumu Solomo yopanga zinthu zotsatirazi panyumba ya Yehova:+
40 Hiramu+ anapanganso mabeseni, mafosholo+ ndi mbale zolowa.+ Choncho iye anamaliza ntchito yonse imene ankagwirira Mfumu Solomo yopanga zinthu zotsatirazi panyumba ya Yehova:+