1 Mafumu 7:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 zipilala ziwiri,+ mitu ya zipilala yooneka ngati mbale zolowa imene anaiika pamwamba pa zipilala ziwirizo ndi maukonde awiri+ okutira mitu iwiri imene inali pamwamba pa zipilalazo.
41 zipilala ziwiri,+ mitu ya zipilala yooneka ngati mbale zolowa imene anaiika pamwamba pa zipilala ziwirizo ndi maukonde awiri+ okutira mitu iwiri imene inali pamwamba pa zipilalazo.