1 Mafumu 7:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Solomo sanayeze kulemera kwa ziwiya zonse chifukwa zinali zambiri. Kopayo sanadziwike kulemera kwake.+
47 Solomo sanayeze kulemera kwa ziwiya zonse chifukwa zinali zambiri. Kopayo sanadziwike kulemera kwake.+