1 Mafumu 7:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Anapanganso zoikapo nyale+ zagolide woyenga bwino ndipo anaziika pafupi ndi chipinda chamkati, anaika 5 kumanja, 5 kumanzere. Ndiponso anapanga maluwa agolide,+ nyale zagolide, zopanira zagolide zozimitsira nyale,+
49 Anapanganso zoikapo nyale+ zagolide woyenga bwino ndipo anaziika pafupi ndi chipinda chamkati, anaika 5 kumanja, 5 kumanzere. Ndiponso anapanga maluwa agolide,+ nyale zagolide, zopanira zagolide zozimitsira nyale,+