1 Mafumu 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho mapiko a akerubiwo anali pamwamba pa Likasa, moti akerubiwo anatchinga pamwamba pa Likasalo ndi mitengo yake yonyamulira.+
7 Choncho mapiko a akerubiwo anali pamwamba pa Likasa, moti akerubiwo anatchinga pamwamba pa Likasalo ndi mitengo yake yonyamulira.+