1 Mafumu 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mitengo yonyamulirayo+ inali yaitali moti nsonga zake zinkaonekera ku Malo Oyera kutsogolo kwa chipinda chamkati, koma sizinkaonekera panja. Mitengoyo idakali pomwepo mpaka lero. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:8 Nsanja ya Olonda,10/15/2001, tsa. 31
8 Mitengo yonyamulirayo+ inali yaitali moti nsonga zake zinkaonekera ku Malo Oyera kutsogolo kwa chipinda chamkati, koma sizinkaonekera panja. Mitengoyo idakali pomwepo mpaka lero.