1 Mafumu 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiponso mʼnyumbamo ndakonzamo malo oika Likasa, lomwe muli pangano+ limene Yehova anapangana ndi makolo athu pamene ankawachotsa mʼdziko la Iguputo.”
21 Ndiponso mʼnyumbamo ndakonzamo malo oika Likasa, lomwe muli pangano+ limene Yehova anapangana ndi makolo athu pamene ankawachotsa mʼdziko la Iguputo.”