1 Mafumu 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atatero anati: “Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli, palibe Mulungu wina wofanana ndi inu+ kumwambako kapena pansi pano. Mumasunga pangano komanso mumasonyeza chikondi chokhulupirika+ kwa anthu amene amakutumikirani ndi mtima wawo wonse.+
23 Atatero anati: “Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli, palibe Mulungu wina wofanana ndi inu+ kumwambako kapena pansi pano. Mumasunga pangano komanso mumasonyeza chikondi chokhulupirika+ kwa anthu amene amakutumikirani ndi mtima wawo wonse.+