1 Mafumu 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Maso anu akhale akuyangʼana nyumba ino masana komanso usiku. Akhale akuyangʼana malo amene munanena kuti, ‘Dzina langa lidzakhala kumeneko,’+ kuti mumvetsere pemphero limene mtumiki wanu angapemphere atayangʼana kumalo ano.+
29 Maso anu akhale akuyangʼana nyumba ino masana komanso usiku. Akhale akuyangʼana malo amene munanena kuti, ‘Dzina langa lidzakhala kumeneko,’+ kuti mumvetsere pemphero limene mtumiki wanu angapemphere atayangʼana kumalo ano.+