1 Mafumu 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 inu mumve muli kumwamba ndipo muchitepo kanthu posonyeza amene ali wolakwa nʼkumubwezera mogwirizana ndi zochita zake komanso musonyeze amene ali wosalakwa nʼkumupatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo chake.+
32 inu mumve muli kumwamba ndipo muchitepo kanthu posonyeza amene ali wolakwa nʼkumubwezera mogwirizana ndi zochita zake komanso musonyeze amene ali wosalakwa nʼkumupatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo chake.+