1 Mafumu 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 inuyo mumve muli kumwambako ndipo anthu anu Aisiraeli, omwenso ndi atumiki anu, muwakhululukire machimo awo popeza mudzawaphunzitsa+ njira yabwino yoti aziyendamo. Mubweretse mvula mʼdziko lanu+ limene munapatsa anthu anu monga cholowa.
36 inuyo mumve muli kumwambako ndipo anthu anu Aisiraeli, omwenso ndi atumiki anu, muwakhululukire machimo awo popeza mudzawaphunzitsa+ njira yabwino yoti aziyendamo. Mubweretse mvula mʼdziko lanu+ limene munapatsa anthu anu monga cholowa.