1 Mafumu 8:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Mʼdzikomo mukagwa njala,+ mliri, mphepo yotentha yowononga mbewu, matenda ambewu a chuku,+ dzombe, ziwala zowononga, mliri wamtundu uliwonse, nthenda yamtundu uliwonse komanso adani awo akawaukira mʼmizinda yawo,+
37 Mʼdzikomo mukagwa njala,+ mliri, mphepo yotentha yowononga mbewu, matenda ambewu a chuku,+ dzombe, ziwala zowononga, mliri wamtundu uliwonse, nthenda yamtundu uliwonse komanso adani awo akawaukira mʼmizinda yawo,+