1 Mafumu 8:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 (popeza adzamva za dzina lanu lalikulu,+ dzanja lanu lamphamvu ndiponso mkono wanu wokonzeka kuthandiza*), ndipo wabwera nʼkupemphera atayangʼana nyumbayi,
42 (popeza adzamva za dzina lanu lalikulu,+ dzanja lanu lamphamvu ndiponso mkono wanu wokonzeka kuthandiza*), ndipo wabwera nʼkupemphera atayangʼana nyumbayi,