1 Mafumu 8:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 (popeza amenewa ndi anthu anu ndi cholowa chanu,+ amene munawatulutsa mu Iguputo,+ kuwachotsa mʼngʼanjo yosungunulira zitsulo).+
51 (popeza amenewa ndi anthu anu ndi cholowa chanu,+ amene munawatulutsa mu Iguputo,+ kuwachotsa mʼngʼanjo yosungunulira zitsulo).+