1 Mafumu 8:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Solomo atamaliza kupemphera kwa Yehova pemphero lonseli ndiponso kupempha chifundo, anachoka patsogolo pa guwa lansembe la Yehova, chifukwa nthawi yonseyi anali atagwada nʼkukweza manja ake mʼmwamba.+
54 Solomo atamaliza kupemphera kwa Yehova pemphero lonseli ndiponso kupempha chifundo, anachoka patsogolo pa guwa lansembe la Yehova, chifukwa nthawi yonseyi anali atagwada nʼkukweza manja ake mʼmwamba.+