1 Mafumu 8:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Kenako mfumu ndi Aisiraeli onsewo anayamba kupereka nsembe zambiri kwa Yehova.+