1 Mafumu 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova anamuuza kuti: “Ndamva pemphero lako ndi pempho lako lopempha chifundo. Ndayeretsa nyumba imene wamangayi poikamo dzina langa mpaka kalekale+ ndipo maso anga ndi mtima wanga zidzakhala mmenemo nthawi zonse.+
3 Yehova anamuuza kuti: “Ndamva pemphero lako ndi pempho lako lopempha chifundo. Ndayeretsa nyumba imene wamangayi poikamo dzina langa mpaka kalekale+ ndipo maso anga ndi mtima wanga zidzakhala mmenemo nthawi zonse.+