1 Mafumu 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ndidzakhazikitsa mpando wako wachifumu mu Isiraeli mpaka kalekale, ngati mmene ndinalonjezera bambo ako Davide kuti, ‘Munthu wa mʼbanja lako sadzachoka pampando wachifumu wa Isiraeli.’+
5 ndidzakhazikitsa mpando wako wachifumu mu Isiraeli mpaka kalekale, ngati mmene ndinalonjezera bambo ako Davide kuti, ‘Munthu wa mʼbanja lako sadzachoka pampando wachifumu wa Isiraeli.’+