1 Mafumu 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ndidzachotsa Aisiraeli mʼdziko limene ndawapatsa+ ndipo nyumba imene ndaiyeretsa chifukwa cha dzina langa, ndidzaichotsa pamaso panga.+ Aisiraeli adzatonzedwa ndi kunyozedwa pakati pa mitundu yonse ya anthu.+
7 ndidzachotsa Aisiraeli mʼdziko limene ndawapatsa+ ndipo nyumba imene ndaiyeretsa chifukwa cha dzina langa, ndidzaichotsa pamaso panga.+ Aisiraeli adzatonzedwa ndi kunyozedwa pakati pa mitundu yonse ya anthu.+