1 Mafumu 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo adzati, ‘Nʼchifukwa chakuti anasiya Yehova Mulungu wawo amene anatulutsa makolo awo mʼdziko la Iguputo ndipo anatenga milungu ina nʼkumaigwadira ndi kuitumikira. Nʼchifukwa chake Yehova anawabweretsera tsoka lonseli.’”+
9 Ndipo adzati, ‘Nʼchifukwa chakuti anasiya Yehova Mulungu wawo amene anatulutsa makolo awo mʼdziko la Iguputo ndipo anatenga milungu ina nʼkumaigwadira ndi kuitumikira. Nʼchifukwa chake Yehova anawabweretsera tsoka lonseli.’”+