1 Mafumu 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Hiramu+ mfumu ya Turo anathandiza Solomo ndi matabwa a mkungudza, matabwa a mitengo yofanana ndi mkungudza komanso golide yense amene Mfumu Solomo ankafuna.+ Choncho Mfumu Solomo anapatsa Hiramu mizinda 20 mʼdera la Galileya. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:11 Nsanja ya Olonda,7/1/2005, tsa. 29
11 Hiramu+ mfumu ya Turo anathandiza Solomo ndi matabwa a mkungudza, matabwa a mitengo yofanana ndi mkungudza komanso golide yense amene Mfumu Solomo ankafuna.+ Choncho Mfumu Solomo anapatsa Hiramu mizinda 20 mʼdera la Galileya.