1 Mafumu 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumu Solomo inagwiritsa ntchito anthu ogwira ntchito yokakamiza+ kuti amange nyumba ya Yehova,+ nyumba* yake, Chimulu cha Dothi,*+ mpanda wa Yerusalemu ndiponso mzinda wa Hazori,+ wa Megido+ ndi wa Gezeri.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:15 Nsanja ya Olonda,8/15/1988, ptsa. 24-262/15/1986, tsa. 23
15 Mfumu Solomo inagwiritsa ntchito anthu ogwira ntchito yokakamiza+ kuti amange nyumba ya Yehova,+ nyumba* yake, Chimulu cha Dothi,*+ mpanda wa Yerusalemu ndiponso mzinda wa Hazori,+ wa Megido+ ndi wa Gezeri.+