1 Mafumu 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 (Mʼmbuyomo, Farao mfumu ya Iguputo anabwera nʼkulanda mzinda wa Gezeri ndipo anautentha ndi moto. Komanso anapha Akanani+ okhala mumzindawo. Kenako anaupereka kwa mwana wake wamkazi+ monga mphatso pamene ankakwatiwa ndi Solomo.)
16 (Mʼmbuyomo, Farao mfumu ya Iguputo anabwera nʼkulanda mzinda wa Gezeri ndipo anautentha ndi moto. Komanso anapha Akanani+ okhala mumzindawo. Kenako anaupereka kwa mwana wake wamkazi+ monga mphatso pamene ankakwatiwa ndi Solomo.)