1 Mafumu 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Panalinso Aamori onse otsala, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi,+ amene sanali Aisiraeli,+