1 Mafumu 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 komanso mbadwa zawo zimene zinatsala mʼdzikomo, zomwe Aisiraeli analephera kuzipha. Anthu onsewa Solomo ankawagwiritsa ntchito yaukapolo ndipo akupitiriza kugwira ntchito yaukapoloyi mpaka lero.+
21 komanso mbadwa zawo zimene zinatsala mʼdzikomo, zomwe Aisiraeli analephera kuzipha. Anthu onsewa Solomo ankawagwiritsa ntchito yaukapolo ndipo akupitiriza kugwira ntchito yaukapoloyi mpaka lero.+