1 Mafumu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma palibe Aisiraeli amene Solomo anawasandutsa akapolo,+ chifukwa iwo anali asilikali ake, atumiki ake, akalonga ake, asilikali othandiza pa magaleta ndiponso atsogoleri a asilikali ake oyendetsa magaleta ndi amuna okwera pamahatchi.
22 Koma palibe Aisiraeli amene Solomo anawasandutsa akapolo,+ chifukwa iwo anali asilikali ake, atumiki ake, akalonga ake, asilikali othandiza pa magaleta ndiponso atsogoleri a asilikali ake oyendetsa magaleta ndi amuna okwera pamahatchi.