1 Mafumu 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Panali akuluakulu oyangʼanira nduna okwana 550 amene ankayangʼanira ntchito ya Solomo. Iwowa ankayangʼanira anthu ogwira ntchito.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:23 Nsanja ya Olonda,12/1/2005, tsa. 19
23 Panali akuluakulu oyangʼanira nduna okwana 550 amene ankayangʼanira ntchito ya Solomo. Iwowa ankayangʼanira anthu ogwira ntchito.+