1 Mafumu 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mwana wamkazi+ wa Farao anachoka mu Mzinda wa Davide+ nʼkukakhala kunyumba yake imene Solomo anamʼmangira. Kenako Solomo anamanga Chimulu cha Dothi.*+
24 Mwana wamkazi+ wa Farao anachoka mu Mzinda wa Davide+ nʼkukakhala kunyumba yake imene Solomo anamʼmangira. Kenako Solomo anamanga Chimulu cha Dothi.*+