-
1 Mafumu 10:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Koma sindinakhulupirire zimene ndinauzidwa mpaka pamene ndabwera nʼkuona ndi maso anga. Panopa ndaona kuti zimene ndinauzidwa zinali hafu chabe. Nzeru zanu ndi ulemerero wanu zaposa kwambiri zinthu zimene ndinamva.
-