1 Mafumu 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atamandike Yehova Mulungu wanu,+ amene wasangalala nanu nʼkukuikani pampando wachifumu wa Isiraeli. Chifukwa Yehova adzakonda Isiraeli mpaka kalekale, wakuikani kuti mukhale mfumu kuti muziweruza anthu ndi kuchita chilungamo.” 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:9 Nsanja ya Olonda,11/1/1999, tsa. 20
9 Atamandike Yehova Mulungu wanu,+ amene wasangalala nanu nʼkukuikani pampando wachifumu wa Isiraeli. Chifukwa Yehova adzakonda Isiraeli mpaka kalekale, wakuikani kuti mukhale mfumu kuti muziweruza anthu ndi kuchita chilungamo.”