1 Mafumu 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zombo za Hiramu zimene zinkanyamula golide kuchokera ku Ofiri+ zinkabweretsanso matabwa a mtengo wa mʼbawa+ ochuluka kwambiri ndiponso miyala yamtengo wapatali.+
11 Zombo za Hiramu zimene zinkanyamula golide kuchokera ku Ofiri+ zinkabweretsanso matabwa a mtengo wa mʼbawa+ ochuluka kwambiri ndiponso miyala yamtengo wapatali.+