1 Mafumu 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anapanganso zishango 300 zingʼonozingʼono* za golide wosakaniza ndi zitsulo zina. (Chishango chilichonse anachikuta ndi golide wolemera ma mina* atatu.) Kenako mfumuyo inaika zishangozi mʼnyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni.+
17 Anapanganso zishango 300 zingʼonozingʼono* za golide wosakaniza ndi zitsulo zina. (Chishango chilichonse anachikuta ndi golide wolemera ma mina* atatu.) Kenako mfumuyo inaika zishangozi mʼnyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni.+