1 Mafumu 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Panali masitepe 6 okafika kumpando wachifumuwo. Pamwamba pa mpandowo panali kanthu kozungulira kokhala ngati denga. Mpandowo unali ndi moika manja mbali zonse ziwiri. Mʼmbali mwake munali zifaniziro ziwiri za mikango+ itaimirira.
19 Panali masitepe 6 okafika kumpando wachifumuwo. Pamwamba pa mpandowo panali kanthu kozungulira kokhala ngati denga. Mpandowo unali ndi moika manja mbali zonse ziwiri. Mʼmbali mwake munali zifaniziro ziwiri za mikango+ itaimirira.